Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 14:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ndiyeno pa tsiku lachinayi anayamba kuuza mkazi wa Samisoni kuti: “Umunyengerere mwamuna wako kuti atiuze tanthauzo la mwambiwu.+ Akapanda kutiuza, tikutentha ndi moto pamodzi ndi nyumba ya bambo ako.+ Kodi anthu inu mwatiitana kuti mutilande katundu wathu?”+

  • Oweruza 15:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Zitatero, Afilisiti anayamba kufunsa kuti: “Wachita zimenezi ndani?” Ndiyeno iwo anati: “Ndi Samisoni, mkamwini wa munthu wa ku Timuna uja, chifukwa chakuti anatenga mkazi wake ndi kum’pereka kwa mwamuna amene anali mnzake wa mkwati.”+ Choncho Afilisiti anapita kukatentha ndi moto mtsikanayo pamodzi ndi bambo ake.+

  • 2 Mbiri 25:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Chotero Amaziya anapatula asilikali amene anabwera kwa iye kuchokera ku Efuraimu n’kuwauza kuti abwerere kwawo. Koma asilikaliwo anawakwiyira kwambiri Ayuda moti anabwerera kwawo ali okwiya kwambiri.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena