-
2 Samueli 19:43Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
43 Koma anthu a ku Isiraeli anayankha anthu a ku Yuda kuti: “Ifetu tili ndi mafuko 10 mu ufumu umenewu.+ Choncho mu ufumu wa Davide tilitu ndi mphamvu zambiri kuposa inu. Ndiyeno n’chifukwa chiyani mukutinyoza chotero, ndipo kodi ife sitinayenera kukhala patsogolo+ pobweretsa mfumu yathu?” Koma mawu a anthu a ku Yuda anali aukali kwambiri kuposa a anthu a ku Isiraeli.
-