1 Mafumu 11:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Atatero, anamuuza Yerobowamu kuti: “Tengapo zidutswa 10, pakuti Yehova Mulungu wa Isiraeli wati, ‘Ndikung’amba ufumuwu kuuchotsa m’manja mwa Solomo, ndipo iwe ndidzakupatsa mafuko 10.+ 1 Mafumu 12:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Aisiraeli onse ataona kuti mfumuyo sinawamvere, anaiyankha kuti: “Tili ndi gawo lanji mwa Davide?+ Ife tilibe cholowa mwa mwana wa Jese. Pitani kwa milungu yanu+ Aisiraeli. Tsopano iwe Davide,+ uzisamalira nyumba yako yokha.” Aisiraeliwo atatero, anayamba kubwerera kumahema awo.
31 Atatero, anamuuza Yerobowamu kuti: “Tengapo zidutswa 10, pakuti Yehova Mulungu wa Isiraeli wati, ‘Ndikung’amba ufumuwu kuuchotsa m’manja mwa Solomo, ndipo iwe ndidzakupatsa mafuko 10.+
16 Aisiraeli onse ataona kuti mfumuyo sinawamvere, anaiyankha kuti: “Tili ndi gawo lanji mwa Davide?+ Ife tilibe cholowa mwa mwana wa Jese. Pitani kwa milungu yanu+ Aisiraeli. Tsopano iwe Davide,+ uzisamalira nyumba yako yokha.” Aisiraeliwo atatero, anayamba kubwerera kumahema awo.