Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mlaliki 4:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ineyo ndaona ntchito yonse imene anthu amaigwira mwakhama ndiponso imene amaigwira bwino,+ kuti imabweretsa mpikisano pakati pa anthu.*+ Izinso n’zachabechabe ndipo zili ngati kuthamangitsa mphepo.

  • Luka 22:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Komanso, panabuka mkangano woopsa pakati pawo za amene anali kuoneka wamkulu kwambiri.+

  • Luka 22:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Inu musakhale otero.+ Koma amene ali wamkulu kwambiri pa nonsenu akhale ngati wamng’ono kwambiri pa nonsenu,+ ndipo amene ali mtsogoleri akhale wotumikira.+

  • Agalatiya 5:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Tisakhale odzikuza, oyambitsa mpikisano+ pakati pathu, ndi ochitirana kaduka.+

  • Afilipi 2:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Musachite chilichonse ndi mtima wokonda mikangano+ kapena wodzikuza,+ koma modzichepetsa, ndi kuona ena kukhala okuposani.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena