Mateyu 23:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma wamkulu kwambiri pakati panu akhale mtumiki wanu.+ Aefeso 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Muziyenda modzichepetsa nthawi zonse,+ mofatsa, moleza mtima,+ ndiponso mololerana m’chikondi.+ Aefeso 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Gonjeranani+ poopa Khristu.