Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 20:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Sizili choncho pakati panu,+ koma aliyense wofuna kukhala wamkulu pakati panu ayenera kukhala mtumiki wanu.+

  • Maliko 10:43
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 43 Sizili choncho pakati panu. Koma aliyense wofuna kukhala wamkulu pakati panu ayenera kukhala mtumiki wanu.+

  • Luka 9:48
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 48 Ndiyeno anawauza kuti: “Aliyense wolandira mwana wamng’ono uyu m’dzina langa walandiranso ine. Ndipo aliyense wolandira ine walandiranso amene anandituma ine.+ Pakuti aliyense wokhala ngati wamng’ono+ pakati pa nonsenu ndi amene ali wamkulu.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena