Mateyu 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chotero, aliyense amene adzadzichepetsa+ ngati mwana wamng’ono uyu ndi amene adzakhala wamkulu kwambiri mu ufumu wakumwamba.+ Mateyu 23:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma wamkulu kwambiri pakati panu akhale mtumiki wanu.+ Maliko 10:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Sizili choncho pakati panu. Koma aliyense wofuna kukhala wamkulu pakati panu ayenera kukhala mtumiki wanu.+ Luka 22:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Inu musakhale otero.+ Koma amene ali wamkulu kwambiri pa nonsenu akhale ngati wamng’ono kwambiri pa nonsenu,+ ndipo amene ali mtsogoleri akhale wotumikira.+
4 Chotero, aliyense amene adzadzichepetsa+ ngati mwana wamng’ono uyu ndi amene adzakhala wamkulu kwambiri mu ufumu wakumwamba.+
43 Sizili choncho pakati panu. Koma aliyense wofuna kukhala wamkulu pakati panu ayenera kukhala mtumiki wanu.+
26 Inu musakhale otero.+ Koma amene ali wamkulu kwambiri pa nonsenu akhale ngati wamng’ono kwambiri pa nonsenu,+ ndipo amene ali mtsogoleri akhale wotumikira.+