Mateyu 20:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Sizili choncho pakati panu,+ koma aliyense wofuna kukhala wamkulu pakati panu ayenera kukhala mtumiki wanu.+ Mateyu 23:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Aliyense wodzikweza adzatsitsidwa,+ koma aliyense wodzichepetsa adzakwezedwa.+ Luka 14:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti aliyense wodzikweza adzatsitsidwa, ndipo wodzichepetsa adzakwezedwa.”+ Luka 22:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Inu musakhale otero.+ Koma amene ali wamkulu kwambiri pa nonsenu akhale ngati wamng’ono kwambiri pa nonsenu,+ ndipo amene ali mtsogoleri akhale wotumikira.+ Yakobo 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Dzichepetseni pamaso pa Yehova,+ ndipo iye adzakukwezani.+
26 Sizili choncho pakati panu,+ koma aliyense wofuna kukhala wamkulu pakati panu ayenera kukhala mtumiki wanu.+
26 Inu musakhale otero.+ Koma amene ali wamkulu kwambiri pa nonsenu akhale ngati wamng’ono kwambiri pa nonsenu,+ ndipo amene ali mtsogoleri akhale wotumikira.+