Genesis 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 koma sanakondwere naye Kaini ndi nsembe yake+ m’pang’ono pomwe. Chotero Kaini anapsa mtima kwambiri+ ndipo nkhope yake inagwa. Mateyu 27:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pakuti iye anadziwa kuti anamupereka chifukwa cha kaduka.+ Agalatiya 5:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Tisakhale odzikuza, oyambitsa mpikisano+ pakati pathu, ndi ochitirana kaduka.+ Yakobo 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kapena mukuyesa kuti lemba limanena pachabe kuti: “Mzimu umene uli mwa ife uli ndi chizolowezi cholakalaka zinthu zosiyanasiyana”?+ 1 Yohane 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 osati ngati Kaini, amene anachokera kwa woipayo n’kupha+ m’bale wake. N’chifukwa chiyani iye anapha m’bale wake? Chifukwa chakuti zochita zake zinali zoipa,+ koma za m’bale wake zinali zolungama.+
5 koma sanakondwere naye Kaini ndi nsembe yake+ m’pang’ono pomwe. Chotero Kaini anapsa mtima kwambiri+ ndipo nkhope yake inagwa.
5 Kapena mukuyesa kuti lemba limanena pachabe kuti: “Mzimu umene uli mwa ife uli ndi chizolowezi cholakalaka zinthu zosiyanasiyana”?+
12 osati ngati Kaini, amene anachokera kwa woipayo n’kupha+ m’bale wake. N’chifukwa chiyani iye anapha m’bale wake? Chifukwa chakuti zochita zake zinali zoipa,+ koma za m’bale wake zinali zolungama.+