Miyambo 27:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mkwiyo umasefukira ndipo ukali ndi wankhanza,+ koma nsanje ndani angaipirire?+ Maliko 15:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti iye anadziwa kuti ansembe aakulu anamupereka chifukwa cha kaduka.+ Yohane 12:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pamenepo Afarisi+ anayamba kuuzana kuti: “Apa ndiye mukudzionera nokha kuti palibiretu chimene tikuphulapo. Onani! Dziko lonse lakhamukira kwa iye.”+ Aroma 1:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 popeza anadzazidwa ndi zosalungama+ zonse, kuipa+ konse, kusirira konse kwa nsanje,+ ndi uchimo+ wonse. Mtima wawo unadzala kaduka,+ umbanda,+ ndewu,+ chinyengo+ ndi njiru.+ Anakonda manong’onong’o+
19 Pamenepo Afarisi+ anayamba kuuzana kuti: “Apa ndiye mukudzionera nokha kuti palibiretu chimene tikuphulapo. Onani! Dziko lonse lakhamukira kwa iye.”+
29 popeza anadzazidwa ndi zosalungama+ zonse, kuipa+ konse, kusirira konse kwa nsanje,+ ndi uchimo+ wonse. Mtima wawo unadzala kaduka,+ umbanda,+ ndewu,+ chinyengo+ ndi njiru.+ Anakonda manong’onong’o+