Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mlaliki 4:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ineyo ndaona ntchito yonse imene anthu amaigwira mwakhama ndiponso imene amaigwira bwino,+ kuti imabweretsa mpikisano pakati pa anthu.*+ Izinso n’zachabechabe ndipo zili ngati kuthamangitsa mphepo.

  • 1 Akorinto 4:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Kodi akukupangitsa kukhala wosiyana+ ndi ena ndani? Inde, uli ndi chiyani chimene sunachite kulandira?+ Ndiye ngati unachita kulandira zinthu zimenezo,+ n’chifukwa chiyani ukudzitama+ ngati kuti sunachite kulandira?

  • Agalatiya 6:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Koma aliyense payekha ayese ntchito yake, kuti aone kuti ndi yotani.+ Akatero adzakhala ndi chifukwa chosangalalira ndi ntchito yake, osati modziyerekezera+ ndi munthu wina.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena