-
Oweruza 15:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Zitatero, Afilisiti anayamba kufunsa kuti: “Wachita zimenezi ndani?” Ndiyeno iwo anati: “Ndi Samisoni, mkamwini wa munthu wa ku Timuna uja, chifukwa chakuti anatenga mkazi wake ndi kum’pereka kwa mwamuna amene anali mnzake wa mkwati.”+ Choncho Afilisiti anapita kukatentha ndi moto mtsikanayo pamodzi ndi bambo ake.+
-