Salimo 91:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mulungu wanena kuti: “Popeza wasonyeza kuti amandikonda,+Inenso ndidzamupulumutsa.+Ndidzamuteteza chifukwa wadziwa dzina langa.+ Yohane 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti moyo wosatha+ adzaupeza akamaphunzira ndi kudziwa+ za inu, Mulungu yekhayo amene ali woona,+ ndi za Yesu Khristu, amene inu munamutuma.+ 1 Akorinto 1:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 kuti zikhale monga Malemba amanenera kuti: “Amene akudzitama, adzitame mwa Yehova.”+
14 Mulungu wanena kuti: “Popeza wasonyeza kuti amandikonda,+Inenso ndidzamupulumutsa.+Ndidzamuteteza chifukwa wadziwa dzina langa.+
3 Pakuti moyo wosatha+ adzaupeza akamaphunzira ndi kudziwa+ za inu, Mulungu yekhayo amene ali woona,+ ndi za Yesu Khristu, amene inu munamutuma.+