Salimo 99:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye amakonda chilungamo ngati mmene mfumu yamphamvu imachitira.+Inu mwakhazikitsa kulungama.+Mwakhazikitsa chiweruzo ndi chilungamo pakati pa ana a Yakobo.+ Hoseya 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti ndimakondwera ndi kukoma mtima kosatha,+ osati ndi nsembe.+ Ndimakondweranso ndi kudziwa Mulungu, osati ndi nsembe zopsereza zathunthu.+ Mika 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwe munthu wochokera kufumbi, iye anakuuza zimene zili zabwino.+ Kodi Yehova akufuna chiyani kwa iwe? Iye akufuna kuti uzichita chilungamo,+ ukhale wokoma mtima+ ndiponso uziyenda modzichepetsa+ ndi Mulungu wako.+ Mika 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kodi pali Mulungu winanso wofanana ndi inu+ amene amakhululukira zolakwa+ ndi machimo a anthu ake otsala omwe ndi cholowa chake?+ Inu simudzakhalabe wokwiya mpaka kalekale, pakuti kusonyeza kukoma mtima kosatha kumakusangalatsani.+
4 Iye amakonda chilungamo ngati mmene mfumu yamphamvu imachitira.+Inu mwakhazikitsa kulungama.+Mwakhazikitsa chiweruzo ndi chilungamo pakati pa ana a Yakobo.+
6 Pakuti ndimakondwera ndi kukoma mtima kosatha,+ osati ndi nsembe.+ Ndimakondweranso ndi kudziwa Mulungu, osati ndi nsembe zopsereza zathunthu.+
8 Iwe munthu wochokera kufumbi, iye anakuuza zimene zili zabwino.+ Kodi Yehova akufuna chiyani kwa iwe? Iye akufuna kuti uzichita chilungamo,+ ukhale wokoma mtima+ ndiponso uziyenda modzichepetsa+ ndi Mulungu wako.+
18 Kodi pali Mulungu winanso wofanana ndi inu+ amene amakhululukira zolakwa+ ndi machimo a anthu ake otsala omwe ndi cholowa chake?+ Inu simudzakhalabe wokwiya mpaka kalekale, pakuti kusonyeza kukoma mtima kosatha kumakusangalatsani.+