Ekisodo 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndi mulungu wina uti amene angafanane nanu, inu Yehova?+Ndinu woyera kopambana, ndani angafanane ndi inu?+Ndinu woyenera kuopedwa+ ndi kukuimbirani nyimbo zotamanda.+ Inu ndinu wochita zodabwitsa.+ Salimo 99:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwo atamande dzina lanu.+Dzina lanu ndi lalikulu, lochititsa mantha ndi loyera.+ Luka 1:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Chifukwa Wamphamvuyo wandichitira zazikulu, ndipo dzina lake ndi loyera.+
11 Ndi mulungu wina uti amene angafanane nanu, inu Yehova?+Ndinu woyera kopambana, ndani angafanane ndi inu?+Ndinu woyenera kuopedwa+ ndi kukuimbirani nyimbo zotamanda.+ Inu ndinu wochita zodabwitsa.+