Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 50:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Inu munali ndi cholinga chondichitira zoipa. Koma Mulungu anali ndi cholinga chabwino, kuti apulumutse miyoyo ya anthu ambiri ngati mmene akuchitira panomu.+

  • Salimo 126:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Amene akupita kumunda akulira,+

      Atasenza thumba lodzaza mbewu,+

      Adzabwerako akufuula mosangalala,+

      Atasenza mtolo wake wa zokolola.+

  • Mlaliki 7:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Mbiri yabwino imaposa mafuta onunkhira,+ ndipo tsiku lomwalira limaposa tsiku lobadwa.+

  • Yohane 12:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Ndithudi ndikukuuzani, Kambewu ka tirigu kakapanda kugwa m’nthaka ndi kufa, kamakhalabe kamodzi komweko. Koma kakafa,+ kamadzabala zipatso zambiri.

  • Yakobo 5:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Monga mmene mukudziwira, anthu amene anapirira timawatcha odala.+ Munamva za kupirira kwa Yobu+ ndipo mwaona zimene Yehova anamupatsa,+ mwaona kuti Yehova ndi wachikondi chachikulu ndi wachifundo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena