Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mlaliki 7:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Mapeto a chinthu amakhala bwino kuposa chiyambi chake,+ ndipo munthu woleza mtima ndi wabwino kuposa munthu wodzikuza.+

  • 2 Akorinto 5:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Tikudziwa kuti nyumba yathu ya padziko lapansi pano,+ msasa uno,+ ikadzaphwasuka,+ tidzalandira nyumba yochokera kwa Mulungu. Imeneyo idzakhala nyumba yosamangidwa ndi manja,+ koma yamuyaya,+ ndipo idzakhala kumwamba.

  • Chivumbulutso 2:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Usachite mantha ndi mavuto amene ukumane nawo.+ Taona! Mdyerekezi+ adzapitiriza kuponya m’ndende ena a inu, kuti muyesedwe mpaka pamapeto,+ ndipo mudzakhala m’masautso+ masiku 10. Sonyeza kukhulupirika kwako mpaka imfa,+ ndipo ndidzakupatsa mphoto* ya moyo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena