Mlaliki 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pa nthawi imeneyo oyang’anira nyumba+ azidzanjenjemera, amuna amphamvu adzapindika,+ akazi opera ufa+ adzasiya kugwira ntchito chifukwa adzatsala ochepa, akazi oyang’ana pawindo+ azidzaona mdima, 2 Akorinto 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Komabe, tili ndi chuma+ chimenechi m’zonyamulira+ zoumbidwa ndi dothi,+ kuti mphamvu+ yoposa yachibadwa ichokere kwa Mulungu,+ osati kwa ife.+
3 Pa nthawi imeneyo oyang’anira nyumba+ azidzanjenjemera, amuna amphamvu adzapindika,+ akazi opera ufa+ adzasiya kugwira ntchito chifukwa adzatsala ochepa, akazi oyang’ana pawindo+ azidzaona mdima,
7 Komabe, tili ndi chuma+ chimenechi m’zonyamulira+ zoumbidwa ndi dothi,+ kuti mphamvu+ yoposa yachibadwa ichokere kwa Mulungu,+ osati kwa ife.+