Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 10:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Anthu akamakumbukira zabwino zimene munthu wolungama anali kuchita, amam’dalitsa,+ koma dzina la anthu oipa lidzawola.+

  • Miyambo 22:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Ndi bwino kusankha dzina labwino kusiyana ndi chuma chochuluka.+ Kulemekezedwa kuli bwino kuposa siliva ndi golide.+

  • Yesaya 56:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 m’nyumba mwanga+ ndiponso mkati mwa makoma anga ndidzawapatsa chipilala chachikumbutso+ ndiponso dzina,+ zomwe ndi zabwino kuposa ana aamuna ndi aakazi.+ Ndidzawapatsa dzina limene silidzatha+ mpaka kalekale.+

  • Ezekieli 36:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 ‘Ndidzayeretsa dzina langa lalikulu+ limene linali kudetsedwa pakati pa mitundu ina ya anthu. Inu munadetsa dzina langalo pakati pa anthu a mitundu ina. Ndikadzayeretsedwa pakati panu, pamaso pa anthu a mitundu inawo, iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.+

  • Mateyu 6:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Koma inu muzipemphera motere:+

      “‘Atate wathu wakumwamba, dzina+ lanu liyeretsedwe.+

  • Luka 10:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Komano, musakondwere ndi zimenezi, kuti mizimu yakugonjerani, koma kondwerani chifukwa mayina+ anu alembedwa kumwamba.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena