Mlaliki 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mbiri yabwino imaposa mafuta onunkhira,+ ndipo tsiku lomwalira limaposa tsiku lobadwa.+