1 Samueli 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Elikana mwamuna wake anati: “Hana, n’chifukwa chiyani ukulira, ndipo n’chifukwa chiyani sukudya? Komanso n’chifukwa chiyani ukupwetekedwa mtima?+ Kodi sindine woposa ana aamuna 10 kwa iwe?”+
8 Ndiyeno Elikana mwamuna wake anati: “Hana, n’chifukwa chiyani ukulira, ndipo n’chifukwa chiyani sukudya? Komanso n’chifukwa chiyani ukupwetekedwa mtima?+ Kodi sindine woposa ana aamuna 10 kwa iwe?”+