Aheberi 11:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Iye anachita zimenezi chifukwa anaona kutonzedwa kwake monga Wodzozedwa* kukhala chuma chochuluka+ kuposa chuma cha Iguputo, pakuti anayang’anitsitsa pamphoto imene adzalandire.+
26 Iye anachita zimenezi chifukwa anaona kutonzedwa kwake monga Wodzozedwa* kukhala chuma chochuluka+ kuposa chuma cha Iguputo, pakuti anayang’anitsitsa pamphoto imene adzalandire.+