Aheberi 10:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Pakuti munasonyeza chifundo kwa amene anali m’ndende, ndipo munalola mokondwa kuti katundu wanu alandidwe,+ podziwa kuti inuyo muli ndi chuma chabwino kuposa pamenepo ndiponso chokhalitsa.+
34 Pakuti munasonyeza chifundo kwa amene anali m’ndende, ndipo munalola mokondwa kuti katundu wanu alandidwe,+ podziwa kuti inuyo muli ndi chuma chabwino kuposa pamenepo ndiponso chokhalitsa.+