Yesaya 44:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Uyu adzati: “Ine ndine wa Yehova.”+ Uyo adzadzitcha dzina la Yakobo,+ ndipo wina adzalemba padzanja lake kuti: “Wa Yehova.” Munthu winanso adzadzipatsa dzina la Isiraeli.’+ Yohane 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Komabe onse amene anamulandira,+ anawapatsa mphamvu zokhala ana a Mulungu,+ chifukwa amenewa anakhulupirira m’dzina lake.+
5 Uyu adzati: “Ine ndine wa Yehova.”+ Uyo adzadzitcha dzina la Yakobo,+ ndipo wina adzalemba padzanja lake kuti: “Wa Yehova.” Munthu winanso adzadzipatsa dzina la Isiraeli.’+
12 Komabe onse amene anamulandira,+ anawapatsa mphamvu zokhala ana a Mulungu,+ chifukwa amenewa anakhulupirira m’dzina lake.+