Ezekieli 28:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Unene kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Iwe Sidoni, ine ndithana nawe+ ndipo ndidzalemekezedwa pakati pako.+ Ndikadzapereka ziweruzo mwa iwe ndi kuyeretsedwa kudzera mwa iwe,+ anthu adzadziwa kuti ine ndine Yehova.+
22 Unene kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Iwe Sidoni, ine ndithana nawe+ ndipo ndidzalemekezedwa pakati pako.+ Ndikadzapereka ziweruzo mwa iwe ndi kuyeretsedwa kudzera mwa iwe,+ anthu adzadziwa kuti ine ndine Yehova.+