Salimo 34:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Yehova ali pafupi ndi anthu a mtima wosweka.+Ndipo odzimvera chisoni mumtima mwawo amawapulumutsa.+ Yesaya 66:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Zinthu zonsezi ndinazipanga ndi dzanja langa, choncho zinakhalapo,”+ akutero Yehova. “Ine ndidzayang’ana munthu amene ali wosautsidwa, wosweka mtima,+ ndiponso wonjenjemera ndi mawu anga.+
18 Yehova ali pafupi ndi anthu a mtima wosweka.+Ndipo odzimvera chisoni mumtima mwawo amawapulumutsa.+
2 “Zinthu zonsezi ndinazipanga ndi dzanja langa, choncho zinakhalapo,”+ akutero Yehova. “Ine ndidzayang’ana munthu amene ali wosautsidwa, wosweka mtima,+ ndiponso wonjenjemera ndi mawu anga.+