Yobu 24:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kukangocha, wakupha amadzukaKupita kukapha wozunzika ndi wosauka,+Ndipo usiku iye amakhala wakuba.+
14 Kukangocha, wakupha amadzukaKupita kukapha wozunzika ndi wosauka,+Ndipo usiku iye amakhala wakuba.+