Mateyu 24:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 “Koma dziwani ichi: Ngati mwininyumba angadziwe nthawi yobwera mbala,+ angakhale maso ndipo sangalole kuti mbala zithyole ndi kulowa m’nyumba mwake. 1 Atesalonika 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti inu eni mukudziwa bwino kuti tsiku la Yehova*+ lidzabwera ndendende ngati mbala usiku.+
43 “Koma dziwani ichi: Ngati mwininyumba angadziwe nthawi yobwera mbala,+ angakhale maso ndipo sangalole kuti mbala zithyole ndi kulowa m’nyumba mwake.