Oweruza 9:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Haa! Anthu awa akanakhala m’manja mwanga,+ ndikanam’chotsa Abimeleki.” Ndiyeno anauza Abimeleki kuti: “Chulukitsa asilikali ako ndipo udzamenyane ndi ine.”+
29 Haa! Anthu awa akanakhala m’manja mwanga,+ ndikanam’chotsa Abimeleki.” Ndiyeno anauza Abimeleki kuti: “Chulukitsa asilikali ako ndipo udzamenyane ndi ine.”+