2 Samueli 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno Abisalomu anali kupitiriza kunena kuti: “Haa! Zikanakhalatu bwino ndikanaikidwa kukhala woweruza m’dziko lino+ kuti munthu aliyense wokhala ndi mlandu kapena wofuna chiweruzo azibwera kwa ine, ndipo ndikanamuchitira chilungamo.”+ Salimo 10:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti woipa amadzitamandira ndi zilakolako zake zadyera,+Ndipo wopanga phindu lachinyengo+ amadzitamanda.נ [Nun]Iye amanyoza Yehova.+ Aroma 1:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 ndi miseche.+ Anakhala odana ndi Mulungu, achipongwe,+ odzikweza,+ odzimva,+ oyambitsa zoipa,+ osamvera makolo,+
4 Ndiyeno Abisalomu anali kupitiriza kunena kuti: “Haa! Zikanakhalatu bwino ndikanaikidwa kukhala woweruza m’dziko lino+ kuti munthu aliyense wokhala ndi mlandu kapena wofuna chiweruzo azibwera kwa ine, ndipo ndikanamuchitira chilungamo.”+
3 Pakuti woipa amadzitamandira ndi zilakolako zake zadyera,+Ndipo wopanga phindu lachinyengo+ amadzitamanda.נ [Nun]Iye amanyoza Yehova.+
30 ndi miseche.+ Anakhala odana ndi Mulungu, achipongwe,+ odzikweza,+ odzimva,+ oyambitsa zoipa,+ osamvera makolo,+