Ekisodo 20:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Usalakelake nyumba ya mnzako. Usalakelake mkazi wa mnzako,+ kapolo wake wamwamuna, kapolo wake wamkazi, ng’ombe yake, bulu wake, kapena chilichonse cha mnzako.”+ Miyambo 25:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Usadzilemekeze wekha pamaso pa mfumu,+ ndipo usaime pamalo a anthu olemekezeka,+ Maliko 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 zachigololo, kusirira kwa nsanje,+ kuchita zoipa, chinyengo, khalidwe lotayirira,+ diso la kaduka, mnyozo, kudzikweza, ndiponso kuchita zinthu mosaganizira ena.
17 “Usalakelake nyumba ya mnzako. Usalakelake mkazi wa mnzako,+ kapolo wake wamwamuna, kapolo wake wamkazi, ng’ombe yake, bulu wake, kapena chilichonse cha mnzako.”+
22 zachigololo, kusirira kwa nsanje,+ kuchita zoipa, chinyengo, khalidwe lotayirira,+ diso la kaduka, mnyozo, kudzikweza, ndiponso kuchita zinthu mosaganizira ena.