Salimo 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iwo amalankhulana zabodza.+Amalankhulana ndi milomo yoshashalika+ komanso ndi mitima iwiri.+ Miyambo 27:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mlendo akutamande, osati pakamwa pako. Munthu wochokera kudziko lina achite zimenezo, osati milomo yako.+ 2 Petulo 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pamene akuwalonjeza ufulu,+ eni akewo ndi akapolo a khalidwe loipa.+ Pakuti aliyense amene wagonjetsedwa, amakhala kapolo kwa womugonjetsayo.+
2 Mlendo akutamande, osati pakamwa pako. Munthu wochokera kudziko lina achite zimenezo, osati milomo yako.+
19 Pamene akuwalonjeza ufulu,+ eni akewo ndi akapolo a khalidwe loipa.+ Pakuti aliyense amene wagonjetsedwa, amakhala kapolo kwa womugonjetsayo.+