Oweruza 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ana a Amoni atayamba kumenyana ndi Aisiraeli,+ akulu a ku Giliyadi anapita mwamsanga kukatenga Yefita kudziko la Tobu.+
5 Ana a Amoni atayamba kumenyana ndi Aisiraeli,+ akulu a ku Giliyadi anapita mwamsanga kukatenga Yefita kudziko la Tobu.+