Oweruza 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo ana a Amoni anali kuwoloka Yorodano kukamenyana ndi fuko la Yuda, la Benjamini, ndi la Efuraimu, moti Isiraeli anasautsika kwambiri.+
9 Ndipo ana a Amoni anali kuwoloka Yorodano kukamenyana ndi fuko la Yuda, la Benjamini, ndi la Efuraimu, moti Isiraeli anasautsika kwambiri.+