Yoswa 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Maere achitatu+ anagwera ana a Zebuloni+ potsata mabanja awo. Malire a cholowa chawo anayambira ku Saridi Yoswa 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 komanso ku Katati, Nahalala, Simironi,+ Idala, ndi ku Betelehemu.+ Mizindayi inalipo 12 ndi midzi yake.
10 Maere achitatu+ anagwera ana a Zebuloni+ potsata mabanja awo. Malire a cholowa chawo anayambira ku Saridi
15 komanso ku Katati, Nahalala, Simironi,+ Idala, ndi ku Betelehemu.+ Mizindayi inalipo 12 ndi midzi yake.