Oweruza 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno tsiku lina, mngelo wa Yehova anaonekera kwa mkaziyo+ ndi kumuuza kuti: “Tamvera, panopa ndiwe wosabereka ndipo ulibe mwana. Koma udzatenga pakati ndi kubereka mwana wamwamuna.+
3 Ndiyeno tsiku lina, mngelo wa Yehova anaonekera kwa mkaziyo+ ndi kumuuza kuti: “Tamvera, panopa ndiwe wosabereka ndipo ulibe mwana. Koma udzatenga pakati ndi kubereka mwana wamwamuna.+