Ekisodo 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno Mose anauza Yehova kuti: “Pepani Yehova, ine sinditha kulankhula, kuyambira kalekale, kapena pamene mwalankhula ndi ine mtumiki wanu. Pakuti ndimalankhula movutikira ndipo ndine wa lilime lolemera.”+ Oweruza 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma iye anayankha kuti: “Pepani Yehova. Kodi Isiraeli ndidzam’pulumutsa ndi chiyani?+ Pajatu banja lathu* ndilo laling’ono zedi m’fuko lonse la Manase, ndipo m’nyumba ya bambo anga, wamng’ono kwambiri ndine.”+
10 Ndiyeno Mose anauza Yehova kuti: “Pepani Yehova, ine sinditha kulankhula, kuyambira kalekale, kapena pamene mwalankhula ndi ine mtumiki wanu. Pakuti ndimalankhula movutikira ndipo ndine wa lilime lolemera.”+
15 Koma iye anayankha kuti: “Pepani Yehova. Kodi Isiraeli ndidzam’pulumutsa ndi chiyani?+ Pajatu banja lathu* ndilo laling’ono zedi m’fuko lonse la Manase, ndipo m’nyumba ya bambo anga, wamng’ono kwambiri ndine.”+