Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 34:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Kenako mudzatenga ena mwa ana awo aakazi kuti akhale akazi a ana anu aamuna,+ ndipo ana awo aakazi adzachita chiwerewere ndi milungu yawo, n’kuchititsa ana anu aamuna kuchita chiwerewere ndi milungu yawo.+

  • Deuteronomo 7:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Usadzachite nawo mgwirizano wa ukwati. Usadzapereke ana ako aakazi kwa ana awo aamuna ndipo usadzatenge ana awo aakazi ndi kuwapereka kwa ana ako aamuna.+

  • Nehemiya 13:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Kodi si zodabwitsa kuti inunso mukuchita choipa chachikulu chimenechi, mwa kukwatira akazi achilendo, kumene ndi kuchita mosakhulupirika kwa Mulungu wanu?”+

  • 1 Akorinto 7:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Mkazi ndi womangika pa nthawi yonse imene mwamuna wake ali moyo.+ Komano mwamuna wake akamwalira, mkaziyo ndi womasuka kukwatiwa ndi aliyense amene akufuna, koma akwatiwe mwa Ambuye.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena