Genesis 29:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Usangalale+ mokwanira ndi mkaziyu mlungu wonse wokondwerera ukwati wake. Kenako ndidzakupatsa mkazi winayu, komatu udzandigwirira ntchito zaka zina 7.”+
27 Usangalale+ mokwanira ndi mkaziyu mlungu wonse wokondwerera ukwati wake. Kenako ndidzakupatsa mkazi winayu, komatu udzandigwirira ntchito zaka zina 7.”+