Oweruza 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno patapita nthawi, m’masiku okolola tirigu, Samisoni anapita kukaona mkazi wake uja, atatenga kamwana ka mbuzi.+ Pamenepo iye anati: “Ndilowa m’chipinda cha mkazi wanga.”+ Koma bambo a mkaziyo sanam’lole kuti alowe.
15 Ndiyeno patapita nthawi, m’masiku okolola tirigu, Samisoni anapita kukaona mkazi wake uja, atatenga kamwana ka mbuzi.+ Pamenepo iye anati: “Ndilowa m’chipinda cha mkazi wanga.”+ Koma bambo a mkaziyo sanam’lole kuti alowe.