Genesis 45:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma atamufotokozera mawu onse amene Yosefe ananena, ndiponso ataona ngolo zimene Yosefe anatumiza kuti zidzam’tenge, mtima wa Yakobo bambo awo unayamba kubwereramo.+ 1 Samueli 30:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anamupatsanso chidutswa cha nkhuyu zouma zoumba pamodzi ndi zidutswa ziwiri za mphesa zouma zoumba pamodzi.+ Iye anadya ndipo anapezanso mphamvu,+ chifukwa sanadye mkate kapena kumwa madzi kwa masiku atatu, usana ndi usiku. Yesaya 40:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Iye amapereka mphamvu kwa munthu wotopa,+ ndipo wofooka amam’patsa nyonga zochuluka.+
27 Koma atamufotokozera mawu onse amene Yosefe ananena, ndiponso ataona ngolo zimene Yosefe anatumiza kuti zidzam’tenge, mtima wa Yakobo bambo awo unayamba kubwereramo.+
12 Anamupatsanso chidutswa cha nkhuyu zouma zoumba pamodzi ndi zidutswa ziwiri za mphesa zouma zoumba pamodzi.+ Iye anadya ndipo anapezanso mphamvu,+ chifukwa sanadye mkate kapena kumwa madzi kwa masiku atatu, usana ndi usiku.