Oweruza 16:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 (Pa nthawiyi m’nyumbamo munadzaza amuna ndi akazi, ndipo olamulira onse ogwirizana a Afilisiti anali mmenemo.+ Padenga la nyumbayo panali amuna ndi akazi pafupifupi 3,000 amene anali kuonerera Samisoni akuchita zoseketsa.)+ Yobu 31:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kodi si paja wochita zoipa amakumana ndi zosautsa,+Ndipo ochitira anzawo zopweteka tsoka limawagwera?
27 (Pa nthawiyi m’nyumbamo munadzaza amuna ndi akazi, ndipo olamulira onse ogwirizana a Afilisiti anali mmenemo.+ Padenga la nyumbayo panali amuna ndi akazi pafupifupi 3,000 amene anali kuonerera Samisoni akuchita zoseketsa.)+
3 Kodi si paja wochita zoipa amakumana ndi zosautsa,+Ndipo ochitira anzawo zopweteka tsoka limawagwera?