Ekisodo 20:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako+ kuti masiku ako atalike m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa.+ Ekisodo 20:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Usabe.+ Levitiko 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 iye akachimwa mwa njira imeneyi, ndipo wapalamuladi,+ azibweza zinthu zimene anafwambazo, kapena zinthu zimene analanda mwachinyengo, kapena chimene chili m’manja mwake chimene anam’sungitsa, kapena chinthu chotayika chimene anatola,
12 “Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako+ kuti masiku ako atalike m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa.+
4 iye akachimwa mwa njira imeneyi, ndipo wapalamuladi,+ azibweza zinthu zimene anafwambazo, kapena zinthu zimene analanda mwachinyengo, kapena chimene chili m’manja mwake chimene anam’sungitsa, kapena chinthu chotayika chimene anatola,