Oweruza 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kuwonjezera apo, Mika anapatsa mphamvu Mleviyo+ kuti atumikire monga wansembe+ wake ndi kupitiriza kukhala m’nyumba ya Mika. Oweruza 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Poyankha iye anati: “Mika anagwirizana ndi ine kuti andilembe ntchito,+ ndi cholinga choti ndizitumikira monga wansembe+ wake.”
12 Kuwonjezera apo, Mika anapatsa mphamvu Mleviyo+ kuti atumikire monga wansembe+ wake ndi kupitiriza kukhala m’nyumba ya Mika.
4 Poyankha iye anati: “Mika anagwirizana ndi ine kuti andilembe ntchito,+ ndi cholinga choti ndizitumikira monga wansembe+ wake.”