Oweruza 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Atatero Mika anamuuza kuti: “Ukhale ndi ine ndipo uzitumikira ngati tate+ ndi wansembe+ wanga. Ine ndizikupatsa ndalama zasiliva 10 pa chaka, komanso zovala zako zoyenera ndi chakudya.” Pamenepo Mleviyo analowa m’nyumbamo. Mika 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Atsogoleri a mumzindawo saweruza asanalandire chiphuphu+ ndipo ansembe ake amaphunzitsa kuti apeze malipiro.+ Aneneri ake amalosera kuti apeze ndalama.+ Komatu iwo amadalira Yehova ndipo amanena kuti: “Kodi Yehova sali pakati pathu?+ Choncho tsoka silidzatigwera.”+
10 Atatero Mika anamuuza kuti: “Ukhale ndi ine ndipo uzitumikira ngati tate+ ndi wansembe+ wanga. Ine ndizikupatsa ndalama zasiliva 10 pa chaka, komanso zovala zako zoyenera ndi chakudya.” Pamenepo Mleviyo analowa m’nyumbamo.
11 Atsogoleri a mumzindawo saweruza asanalandire chiphuphu+ ndipo ansembe ake amaphunzitsa kuti apeze malipiro.+ Aneneri ake amalosera kuti apeze ndalama.+ Komatu iwo amadalira Yehova ndipo amanena kuti: “Kodi Yehova sali pakati pathu?+ Choncho tsoka silidzatigwera.”+