Genesis 45:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chotero si inu amene munanditumiza kuno,+ koma Mulungu woona. Anachita zimenezi kuti andiike kukhala tate+ kwa Farao, ndi mbuye wa nyumba yake yonse, ndiponso woyang’anira wa dziko lonse la Iguputo. 2 Mafumu 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mfumu ya Isiraeli itangoona anthuwo, inafunsa Elisa kuti: “Kodi ndiwaphe?+ Ndiwaphe kodi bambo?”+ Yesaya 22:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iyeyo ndidzamuveka mkanjo wako ndipo lamba wako ndidzamumanga mwamphamvu m’chiuno mwake.+ Ulamuliro wako ndidzaupereka m’manja mwake ndipo iye adzakhala tate wa anthu okhala mu Yerusalemu ndi a m’nyumba ya Yuda.+
8 Chotero si inu amene munanditumiza kuno,+ koma Mulungu woona. Anachita zimenezi kuti andiike kukhala tate+ kwa Farao, ndi mbuye wa nyumba yake yonse, ndiponso woyang’anira wa dziko lonse la Iguputo.
21 Iyeyo ndidzamuveka mkanjo wako ndipo lamba wako ndidzamumanga mwamphamvu m’chiuno mwake.+ Ulamuliro wako ndidzaupereka m’manja mwake ndipo iye adzakhala tate wa anthu okhala mu Yerusalemu ndi a m’nyumba ya Yuda.+