1 Samueli 24:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano ngati munthu wapeza mdani wake, kodi angamulole kupita mwamtendere?+ Chonchotu Yehova adzakufupa ndi zinthu zabwino,+ chifukwa chakuti lero wandichitira zabwino.
19 Tsopano ngati munthu wapeza mdani wake, kodi angamulole kupita mwamtendere?+ Chonchotu Yehova adzakufupa ndi zinthu zabwino,+ chifukwa chakuti lero wandichitira zabwino.