1 Samueli 26:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pamenepo Sauli anauza Davide kuti: “Udalitsike mwana wanga Davide. Mosakayikira iwe udzachita ntchito zazikulu ndipo udzapambana ndithu.”+ Pamenepo Davide anachoka ndipo Sauli anabwerera kwawo.+ 2 Mbiri 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pajatu maso a Yehova+ akuyendayenda padziko lonse lapansi+ kuti aonetse mphamvu zake kwa anthu amene mtima wawo+ uli wathunthu kwa iye. Mwachita zopusa+ pankhani imeneyi, chifukwa kuyambira tsopano anthu azichita nanu nkhondo.”+ Salimo 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yehova amandipatsa mphoto mogwirizana ndi chilungamo changa.+Amandibwezera mogwirizana ndi kuyera kwa manja anga.+
25 Pamenepo Sauli anauza Davide kuti: “Udalitsike mwana wanga Davide. Mosakayikira iwe udzachita ntchito zazikulu ndipo udzapambana ndithu.”+ Pamenepo Davide anachoka ndipo Sauli anabwerera kwawo.+
9 Pajatu maso a Yehova+ akuyendayenda padziko lonse lapansi+ kuti aonetse mphamvu zake kwa anthu amene mtima wawo+ uli wathunthu kwa iye. Mwachita zopusa+ pankhani imeneyi, chifukwa kuyambira tsopano anthu azichita nanu nkhondo.”+
20 Yehova amandipatsa mphoto mogwirizana ndi chilungamo changa.+Amandibwezera mogwirizana ndi kuyera kwa manja anga.+