Mateyu 5:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Koma ine ndikukuuzani kuti: Pitirizani kukonda adani anu+ ndi kupempherera amene akukuzunzani,+ Aroma 12:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Musabwezere choipa pa choipa.+ Chitani zimene anthu onse amaziona kuti ndi zabwino.