Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 41:42
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Atatero, Farao anavula mphete yake yachifumu+ kudzanja lake, n’kuiveka kudzanja la Yosefe. Anamuvekanso malaya amtengo wapatali, ndi tcheni chagolide m’khosi mwake.+

  • 1 Samueli 18:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Pamenepo Yonatani anavula malaya ake akunja odula manja ndi kupatsa Davide. Anam’patsanso zovala zina ngakhalenso lupanga, uta ndi lamba wake.

  • Esitere 8:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ndiyeno Moredekai anachoka pamaso pa mfumu atavala chovala chachifumu+ cha buluu ndi nsalu yoyera. Analinso atavala chisoti chachikulu chachifumu chagolide, mkanjo wa nsalu yabwino kwambiri yaubweya wa nkhosa+ wonyika mu utoto wofiirira.+ Ndipo mumzinda wa Susani munamveka kufuula kwa chisangalalo ndi kukondwera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena